Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 21:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Akayambana amuna, nakakantha mkazi ali ndi pakati, kotero kuti abala, koma alibe kuphwetekwa; alipe ndithu, monga momwe amchulira mwamuna wa mkaziyo; apereke monga anena oweruza.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:22 nkhani