Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 2:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Ndipo Molungu anamva kubuula kwao, ndi Mulungu anakumbukila cipangano cace ndi Abrahamu, ndi Isake, ndi Yakobo.

25. Ndipo Molungu anapenya Aisrayeli, ndi Mulungu anadziwa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 2