Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 2:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pakupita masiku ambiri aja, idafa mfumu ya Aigupto; ndi ana a Israyeli anatsitsa moyo cifukwa ca ukapolo wao, nalira, ndi kulira kwao kunakwera kwa Mulungucifukwa ca ukapolowo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 2

Onani Eksodo 2:23 nkhani