Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 19:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse anabvomera pamodzi, nati, Zonse adazilankhula Yehova tidzazicita. Ndipo Mose anabwera nao mau a anthu kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:8 nkhani