Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 19:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

dzanja liri lonse lisalikhudze, wakulikhudza azimponyatu miyala, kapena kumpyoza; ngakhale coweta ngakhale munthu, zisakhale ndi moyo. Pamene lipenga libanika liu lace azikwera m'phirimo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 19

Onani Eksodo 19:13 nkhani