Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma iwe, dzisankhire mwa anthu ako onse, amuna amtima, akuopa Mulungu, amuna oona, akudana nalo phindu la cinyengo; nuwaikire iwo oterewa, akuru a pa zikwi, akuru a pa mazana, akuru a pa makumi asanu, akuru a pa makumi;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 18

Onani Eksodo 18:21 nkhani