Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 17:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunakhala, pamene Mose anakweza dzanja lace Israyeli analakika; koma pamene anatsitsa dzanja lace Amaleki analakika.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 17

Onani Eksodo 17:11 nkhani