Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 15:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anafika pa Elimu, ndi pamenepo panali akasupe a madzi khumi ndi awiri, ndi akanjedza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamanga cigono cao pomwepo pa madziwo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 15

Onani Eksodo 15:27 nkhani