Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 15:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo anati, Ngati udzamveratu mau a Yehova, Mulungu wako, ndi kucita zoona pamaso pace, ndi kuchera khutu pa malamulo ace, ndi kusunga malemba ace onse, za nthenda zonse ndinaziika pa Aaigupto sindidzaziika pa iwe nnena imodzi; pakuti Ine Yehova ndine wakuciritsa iwe.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 15

Onani Eksodo 15:26 nkhani