Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 15:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anatsogolera Israyeli kucokera ku Nyanja Yofiira, ndipo anaturukako nalowa m'cipululu ca Suri; nayenda m'cipululu masiku atatu, osapeza madzi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 15

Onani Eksodo 15:22 nkhani