Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 14:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Israyeli anaiona nchito yaikuru imene Yehova anacitira Aaigupto, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wace Mose.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:31 nkhani