Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 14:30-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Comweco Yehova anapulumutsa Israyeli tsiku lomwelo m'manja a Aaigupto; ndipo Israyeli anaona Aaigupto akufa m'mphepete mwa nyanja.

31. Ndipo Israyeli anaiona nchito yaikuru imene Yehova anacitira Aaigupto, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wace Mose.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14