Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 14:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anatambasulira dzanja lace kunyanja; ndipo Yehova anabweza nyanja ndi mphepo yolimba ya kum'mawa usiku wonse, naumitsa nyanja; ndipo madziwo anagawikana.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:21 nkhani