Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 14:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Farao anayandikira ana a Israyeli anatukula maso ao, taonani, Aaigupto alinkutsata pambuyo pao; ndipo anaopa kwambiri; ndi ana a Israyeli anapfuulira kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 14

Onani Eksodo 14:10 nkhani