Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 13:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kudzakhala atakulowetsa Yehova m'dziko la Akanani, ndi la Ahiti, ndi la Aamori ndi la Ahivi, ndi la Ayebusi, limene analumbira ndi makolo ako kukupatsa, m'dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi, uzikasunga kutumikira kumeneku mwezi uno.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 13

Onani Eksodo 13:5 nkhani