Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 13:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi kuti,

2. Ndipatulire Ine yense woyamba kubadwa, wotsegulira pa amace mwa ana a Israyeli, mwa anthu ndi mwa zoweta; ndiwo anga.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 13