Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ananena ndi anthu, Kumbukirani tsiku linu limene munaturuka m'Aigupto, m'nyumba ya akapolo; pakuti Yehova anakuturutsani muno ndi dzanja lamphamvu; ndipo asadye kanthu ka cotupitsa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 13

Onani Eksodo 13:3 nkhani