Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 12:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muziidya cotero: okwinda m'cuuno, nsapato zanu pa mapazi anu ndodo yanu m'dzanja lanu, ndipo muziidya msanga; ndiye Paskha wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 12

Onani Eksodo 12:11 nkhani