Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 11:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anawapatsa anthu cisomo pamaso pa Aaigupto. Munthuyo Mose ndiyenso wamkuru ndithu m'dziko la Aigupto, pamaso pa anyamata a Farao, ndi pamaso pa anthu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 11

Onani Eksodo 11:3 nkhani