Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Watsala moo umodzi ndidzamtengera Farao, ndi Aigupto; pambuyo pace adzakulolani mucoke kuno; pamene akulolani kupita, zoonadi adzakuingitsani kuno konse.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 11

Onani Eksodo 11:1 nkhani