Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakucepetsani, nakumvetsani odala, nakudyetsani ndi mana, amene simunawadziwa, angakhale makolo anu sanawadziwa; kuti akudziwitseni kuti munthu sakhala wamoyo ndi mkate wokha, koma munthu akhala wamoyo ndi zonse zakuturuka m'kamwa mwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 8

Onani Deuteronomo 8:3 nkhani