Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti inu ndinu mtundu wa anthu wopatulika wa Yehova Mulungu wanu; Yehova Mulungu wanu anakusankhani, mukhale mtundu wa pa wokha wa iye yekha, mwa mitundu yonse ya anthu akukhala pa nkhope ya dziko.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:6 nkhani