Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma muzicita nao motero: mukapasule maguwa ao a nsembe, ndi kuphwanya zoimiritsa zao, ndi kulikha zifanizo zao, ndi kutentha mafano ao osema ndi moto.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:5 nkhani