Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzatha mitundu yonse ya anthu amene Yehova Mulungu wanu adzapereka kwa inu; diso lanu lisawacitire cifundo; musamatumikira milungu yao; pakuti uku kudzakucitirani msampha.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:16 nkhani