Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 7:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Yehova Mulungu wanu atakulowetsani m'dziko limene mumkako kulilandira likhale lanu lanu, ndipo atakataya amitundu ambiri pamaso panu, Ahiti, ndi Agirigazi, ndi Aamori, ndi Akanani, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi, mitundu isanu ndi iwiri yaikuru ndi yamphamvu yoposa inu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 7

Onani Deuteronomo 7:1 nkhani