Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 6:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Ndipo Yehova anatilamulira tizicita malemba awa onse, kuopa Yehova Mulungu wathu, kuti tipindule nako masiku onse, kuti atisunge amoyo, monga lero lino.

25. Ndipo kudzakhala kwa ife cilungamo, ngati tisamalira kucita malamulo awa onse pamaso pa Yehova Mulungu wathu, monga anatilamuliraife.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6