Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 6:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anatilamulira tizicita malemba awa onse, kuopa Yehova Mulungu wathu, kuti tipindule nako masiku onse, kuti atisunge amoyo, monga lero lino.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6

Onani Deuteronomo 6:24 nkhani