Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 6:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti muope Yehova Mulungu wanu, kusunga malemba ace onse ndi malamulo ace, amene ndikuuzani inu ndi ana anu, ndi zidzukulu zanu, masiku onse a moyo wanu, ndi kuti masiku anu acuruke.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6

Onani Deuteronomo 6:2 nkhani