Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo awa ndi malamulo, malemba, ndi maweruzo, amene Yehova Mulungu wanu analamulira kukuphunzitsani, kuti muziwacita m'dziko limene muolokerako kulilandira;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 6

Onani Deuteronomo 6:1 nkhani