Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 5:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usasirire mkazi wace wa mnzako; usakhumbe nyumba yace ya mnzako, munda wace, kapena wanchito wace wamwamuna, kapena wanchito wace wamkazi, ng'ombe yace, kapena buru wace, kapena kanthu kali konse ka mnzako.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 5

Onani Deuteronomo 5:21 nkhani