Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsikuli munaima pamaso pa Yehova Mulungu wanu m'Horebe muja Yehova anati kwa ine, Ndisonkhanitsire anthu, ndidzawamvetsa mau anga, kuti aphunzire kundiopa Ine masiku ao onse akukhala ndi moyo pa dziko lapansi, ndi kuti aphunzitse ana ao.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 4

Onani Deuteronomo 4:10 nkhani