Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 34:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anakwera kucokera ku zidikha za Moabu, kumka ku phiri la Nebo, pamwamba pa Pisiga, popenyana ndi Yeriko. Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse la Gileadi, kufikira ku Dani;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 34

Onani Deuteronomo 34:1 nkhani