Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 33:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzaitana mitundu ya anthu afike kuphiri;Apo adzaphera nsembe za cilungamo;Popeza adzayamwa zocuruka za m'nyanja,Ndi cuma cobisika mumcenga.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 33

Onani Deuteronomo 33:19 nkhani