Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 31:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Khalani amphamvu, limbikani mitima, musamacita mantha, kapena kuopsedwa cifukwa ca iwowa; popeza Yehova Mulungu wanu ndiye amene amuka nanu; iye sadzakusowani, kapena irukusiyani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:6 nkhani