Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 31:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sonkhanitsan; anthu, amuna ndi akazi ndi ana ang'ono, ndi mlendo wokhala m'midzi mwanu, kuti amve, ndi kuti aphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu, ndi kusamalira kucita mau onse a cilamulo ici;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 31

Onani Deuteronomo 31:12 nkhani