Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 30:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu wanu adzakucurukitsirani nchito zonse za dzanja lanu, zipatso za thupi lanu, ndi zipatso za zoweta zanu, ndi zipatso za nthaka yanu, zikukomereni; popeza Yehova Mulungu wanu adzakondweranso kukucitirani zokoma; monga anakondwera ndi makolo anu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:9 nkhani