Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 30:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mutembenuke ndi kumvera mau a Yehova, ndi kucita malamulo ace onse amene ndikuuzani lero lino.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:8 nkhani