Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 30:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo Yehova Mulungu wanu adzaucotsa ukapolo wanu, ndi kukucitirani cifundo; nadzabwera ndi kukumemezani mwa mitundu yonse ya anthu, kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsiraniko.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:3 nkhani