Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 30:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kukonda Yehova Mulungu wanu, kumvera mau ace, ndi kummamatira iye, tr pakuti iye ndiye moyo wanu, ndi masiku anu ocuruka; kuti mukhale m'dziko limene Yehova analumbirira makolo anu, Abrahamu, Isake, ndi Yakobo, kuwapatsa ili.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:20 nkhani