Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 30:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndicititsa mboni lero kumwamba ndi dziko lapansi zitsutse inu; ndaika pamaso panu moyo ndi imfa, mdalitso ndi temberero; potero, sankhani moyo, kuti mukhale ndi moyo, inu ndi mbeu zanu;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 30

Onani Deuteronomo 30:19 nkhani