Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 3:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

(Pakuti Ogi mfumu ya Basana anatsala yekha wa iwo otsalira Arefai; taonani, kama wace ndiye kama wacitsulo; sukhala kodi m'Raba wa ana a Amoni? utali wace mikono isanu ndi inai, kupingasa kwace mikono inai, kuyesa mkono wa munthu.)

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 3

Onani Deuteronomo 3:11 nkhani