Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 29:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene munafika pamalo pano, Sihoni mfumu ya Hesiboni, ndi Ogi mfumu ya Basana, anaturuka kudzakomana nafe kunkhondo, ndipo tinawakantha;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:7 nkhani