Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 29:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Ndipo Yehova anawazula m'nthaka mwao mokwiya ndi mozaza, ndi m'ukali waukuru, nawaponya m'dziko lina, monga lero lino.

29. Zinsinsi nza Yehova Mulungu wathu; koma zobvumbuluka nza ife ndi ana athu kosatha, kuti ticite mau onse a cilamulo ici.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29