Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 29:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anawazula m'nthaka mwao mokwiya ndi mozaza, ndi m'ukali waukuru, nawaponya m'dziko lina, monga lero lino.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 29

Onani Deuteronomo 29:28 nkhani