Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 28:67 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'mawa mudzati, Mwenzi atafika madzulo! ndi madzulo mudzati, Mwenzi utafika m'mawa! cifukwa ca mantha a m'mtima mwanu amene mudzaopa nao, ndi cifukwa ca zopenya maso anu zimene mudzazipenya.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:67 nkhani