Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 28:49 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yehova adzakutengerani mtundu wa anthu wocokera kutali ku malekezero a dziko lapansi, monga iuluka mphungu; mtundu wa anthu amene simunamva malankhulidwe ao;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 28

Onani Deuteronomo 28:49 nkhani