Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 26:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo kudzali, utakalowa m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale colowa canu, ndipo mwacilandira ndi kukhala m'mwemo;

2. kuti muzitengako zoyamba za zipatso zonse za nthaka, zakubwera nazo inu zocokera m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani; ndi kuziika mumtanga, ndi kupita ku malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kukhalitsako dzina lace.

3. Ndipo mufike kwa wansembe wakukhala m'masiku awa, ndi kunena naye, Ndibvomereza lero lino kwa Yehova Mulungu wako, kuti ndalowa m'dziko limene Yehova analumbirira makolo athu, kuti adzatipatsa ili.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26