Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 26:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti muzitengako zoyamba za zipatso zonse za nthaka, zakubwera nazo inu zocokera m'dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani; ndi kuziika mumtanga, ndi kupita ku malo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha kukhalitsako dzina lace.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 26

Onani Deuteronomo 26:2 nkhani