Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 23:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu wanu sanafuna kumvera Balamu; koma Yehova Mulungu wanu anakusandulizirani tembererolo likhale mdalitso, popeza Yehova Mulungu wanu anakukondani.

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23

Onani Deuteronomo 23:5 nkhani