Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Deuteronomo 23:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Munthu wophwetekwa, wophwanyika kapena wofulika, asalowe m'msonkhano wa Yehova.

2. Mwana wa m'cigololo asalowe m'msonkhano wa Yehova, ngakhale mbadwo wace wakhumi usalowe m'msonkhano wa Yehova.

3. M-amoni kapena Mmoabu asalowe m'msonkhano wa Yehova; ngakhale mbadwo wao wakhumi usalowe m'msonkhano wa Yehova, ku nthawi zonse;

Werengani mutu wathunthu Deuteronomo 23